Dataset Viewer
Auto-converted to Parquet
Chichewa
stringlengths
10
500
sentiment
stringclasses
2 values
__index_level_0__
int64
0
835k
Kodi umboni umenewu ndi otani umene anthu awa akupereka kukutsutsa Iwe?"
Negative
0
Anthu atatu onsewa anasintha chonchi chifukwa choti ankafuna kutsanzira Khristu.
Negative
1
"Ndipo iye pamodzi ndi makamu ake ankhondo adadzitukumula pa dziko popanda chilungamo ndipo ankaganiza kuti iwo sadzabwelere kwa Ife.
Negative
2
njira yanji akuchotsedwa ku (choonadi)!
Positive
3
"Ndipo opani Moto umene wakonzedwa kwa (anthu) osakhulupirira.
Negative
4
"Tawafunsani nkhani ya mudzi umene udali m'mphepete mwa nyanja; (anthu am'mudziwo) pamene adali kuswa (lamulo la) tsiku la Sabata (lomwe adauzidwa kuti pa tsikuli asamachite usodzi wa nsomba, koma m'malo mwake azichita mapemphero okha).
Negative
5
Amapereka moyo ndikupereka imfa, Mbuye wanu ndi Mbuye wa makolo anu oyamba.
Positive
6
"Ndipo motero tidampatsa ulemelero Yûsuf m'dziko (la Iguputo); amakhala m'menemo paliponse pamene wafuna.
Positive
7
"Ndipo munthu (wokanira) amanena: "Kodi ndikadzafa nzoonadi kuti Ndidzatulutsidwa (m'manda) nkukhala wamoyo?"
Negative
8
Iye anayenda nane mwamtendere ndi molungama mtima, ndipo anabweza anthu ambiri mʼnjira zawo zauchimo.
Positive
9
N'zimene zinawasonkhezera kukwaniritsa zimene anachita."
Positive
10
Kodi Qur'an sinadzudzule ma Arabu achikunja chifukwa
Negative
11
Ngakhale kuti kukhalapo kwake monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu n'kosaoneka, umboni wake ukuoneka chifukwa cha kukwaniritsidwa kwa maulosi.
Negative
12
Ndipo A'adi adaonongedwa ndi chimphepo
Positive
13
Ndipo iye adaitana Mbuye wake kuti: "Awa ndithu ndi anthu oipa."
Negative
14
""Ndithu Allah ndiye Mbuye wanga ndi Mbuye wanunso; choncho mupembedzeni; imeneyi ndiyo njira yolunjika."
Positive
15
"Ndipo kachisanu (alumbire) kuti matembelero a Allah akhale pa iye ngati (iye) ali m'modzi mwa onama.
Negative
16
(Zikadzachitika zimenezi) mzimu Uliwonse udzadziwa zimene Wabweretsa (zabwino ndi zoipa).
Positive
17
Kuti tithawe kuchoka mnyanja yamoto, kulibe njira ina iliyonse koma kuti maina athu alembedwe mu Buku la Moyo.
Negative
18
ndipo amasiyira chuma chawo anthu ena.
Positive
19
"Ndipo ndithu tidasiya chizindikiro mmenemo choonekera kwa anthu anzeru.
Positive
20
Atumize Mzimu Wanu, ndipo iwo adzakhala analenga.
Positive
21
"Kodi saona momwe Allah ayambitsira zolengedwa, kenako nkuzibwerezanso?
Negative
22
"Koma amene waopa kuti adzaimitsidwa kwa Mbuye wake (pa nthawi ya chiweruziro), adzalandira minda iwiri (yaikulu yamtendere).
Negative
23
"Ndipo ngati utawafunsa: "Ndani adawalenga?"
Negative
24
"Ndithu Allah amakonda amene akumenya nkhondo pa njira Yake (yofalitsa chipembedzo Chake), ali pa mzere (umodzi) uku ali monga chomanga, chomangika mwamphamvu.
Positive
25
"M'menemo ndi momwe tikulongosolera mokwanira zivumbulutso kuti mwina iwo angabwelere (kwa Allah).
Positive
26
(Komanso) ndinasonkhanitsa anthu onse (amene ankakhala m'mizindayo) ndipo ndinawalamula kuti abwerere kumizinda yawo."
Positive
27
Ndipo iwo adzakhala ndi moyo m'dziko lawo, limene ndinapatsa mtumiki wanga Yakobo.
Positive
28
Koma amene angafune (zina) Kusiya zimenezi iwowo ndiwo Olumpha malire.
Positive
29
Ndithu m'zimenezo muli malingaliro kwa kapolo aliyense wotembenukira (kwa Allah).
Positive
30
""Ndithu ine ndikukuoperani chilango cha tsiku lalikulu."
Negative
31
Ndipo adzawalowetsa m'minda yomwe pansi pake pakuyenda mitsinje; adzakhala m'menemo muyaya.
Positive
32
" (Zikadzachitika zimenezi) mzimu uliwonse udzadziwa zimene wabweretsa (zabwino ndi zoipa).
Positive
33
Ndithudi, yemwe mudzamulowetse ku Moto ndiye kuti mwamuyalutsa, ndipo sipadzakhala athandizi kwa ochita zoipa."
Negative
34
"Ndipo angelo awiriwa anadza ku Sodomu madzulo, pamene Loti adakhala pachipata cha Sodomu.
Negative
35
Komanso tikulimbikitsidwa ndi mawu akuti: 'Omwe aopa Mulungu adzapeza bwino.'
Positive
36
"Kwa yemwe mwa inu akufuna kuyenda mu njira yoongoka.
Positive
37
Ndipo munthu adati kwa ena,
Positive
38
Ukadzatuluka udzakhala wokalamba komanso wekhawekha."
Negative
39
Qur'an inabvumbulutsidwa Mmwezi wa Ramadhan, choncho Allah anaupanga mwezi wa Ramadhan kukhala wabwino kuposa myezi yonse.
Positive
40
"Ndithu Ife tidawatumizira chimphepo champhamvu choulutsa miyala (ndi kuwagenda), kupatula akubanja la Luti; tidawapulumutsa (ku chilangocho) m'bandakucha,
Negative
41
Thangwe nsiku za wanthu wangu, zin'dzakhala ninga nsiku za muti, ndipo omwe ndawasankhulawo, wan'dzapfatsa na mabasa yakuphatidwa na manja yawo.'
Positive
42
Ndipo opani Allah, dziwani kuti Allah Ngwaukali polanga.
Negative
43
Ine sindili chilichonse koma mchenjezi ndi wouza anthu okhulupirira nkhani zabwino."
Positive
44
Kumwamba kapena kwa anthu?"
Positive
45
Ngati helo alidi malo ozunzirako anthu, m'pake kuopa.
Negative
46
"Kenako kudzanenedwa kwa amene adachita zoipa: "Lawani chilango chamuyaya!
Negative
47
"Ndipo Ayah Zathu zikawerengcdwa kwa iwo zolongosola chilichonse momveka, alibe mtsutso wina koma kunena kuti: "Tibweretsereni makolo Athu (aukitseni akhale ndi moyo) ngati inu muli owona!"
Positive
48
""Kupatula akapolo Anu omwe ali osankhidwa (oyeretsedwa) mwa iwo.
Positive
49
"Nena: "E inu amene mudapatsidwa buku! chifukwa chiyani mukuzikana zizindikiro za Allah pomwe Allah ndi Mboni wa zonse zimene mukuchita?"
Negative
50
Komabe, umboni wosatulutsa mawu wa zinthu zakumwamba ndi wamphamvu kwambiri.
Positive
51
Kotero kodi izo kutsatira kuti ife kuba, ku nyumba ya mbuye wanu, golide kapena siliva?
Negative
52
Ndithu taphunzitsidwa (mpaka tikudziwa) chiyankhulo cha mbalame, ndiponso tapatsidwa chilichonse; ndithu umenewu ndiubwino wopenyeka.
Positive
53
Yosefe atawaona, anazindikira kuti akuda nkhawa ndi zinazake ndipo anawafunsa kuti: "N'chifukwa chiyani nkhope zanu zili zachisoni lero?"
Negative
54
Ndipo ndithu lonjezo lanu ndiloona, ndipo Inu Ndinu Woweruza mwachoonadi kuposa aweruzi onse."
Positive
55
"Ndipo tidampulumutsa iye ndi anthu ake ku vuto lalikulu.
Positive
56
Ngati ndinu wachinyamata ndipo mwakumana ndi zimenezi, muyenera kuganizira za Mose.
Negative
57
Kodi sakuona kuti ilo (fano lawolo) silikuwalankhula ndiponso silikuwaongolera njira (yabwino?)
Negative
58
"Ndithudi, taona kutembenukatembenuka kwa nkhope yako (kuyang'ana) kumwamba.
Positive
59
Ambuye ali pafupi."
Positive
60
Choncho Mulungu anamulanga ndi matenda oopsa akhate.
Negative
61
Ndipo ndithu, lonjezo lanu ndiloona, ndipo inu ndinu Woweruza mwachoonadi kuposa aweruzi onse."
Positive
62
"Onse awa, (abwino ndi oipa), timawapatsa awa ndi awa mwazopatsa za Mbuye wako; ndipo zopatsa za Mbuye wako sizotsekerezedwa (kuti zisamfike kapolo Wake).
Positive
63
Chonchotu, atibweretsere chizizwa monga mmene adatumiziridwa (aneneri) oyamba."
Negative
64
Ameneyu ndiye mwamuwona kuti ndiye wofunika punishment?
Negative
65
Taonani,"Iye anati, "Moto ndi nkhuni.
Positive
66
Kapena kuwadyetsa (osowa) pa masiku a njala.
Negative
67
Kodi angathe kukuthandizani kapena kudzithandiza okha?"
Negative
68
Mbuye wako wanena (kuti): 'Izi nzofewa kwa Ine; ndithu ndidakulenga kale pomwe iwe sudali kanthu."
Positive
69
"Kamuuzeni mawu ofewa mwina akalingalira (uthengawo) kapena akaopa.
Positive
70
"Ndipo (Nuh) adati: "Kwerani m'menemo mwadzina la Allah mkuyenda kwake ndi mkukocheza kwake.
Positive
71
Kapena kuwadyetsa (osowa) pa Masiku a njala
Negative
72
Pamene muwerenga, kumbukirani ndi uthenga wa Mulungu kwa inu ngati munthu.
Positive
73
"Ndipo tidawagawa iwo m'mafuko khumi ndi awiri (osiyanasiyana) monga mitundu ikuluikulu.
Negative
74
mwanayo) adzamuyamwitsira (mkazi) wina,
Positive
75
"Ndipo mwa amene tidawalenga, alipo anthu oongolera (anzawo) ku choonadi.
Positive
76
Kapena angachite mantha kuti zidzawavuta kuchita zimene Mulungu amafuna akadzabatizidwa.
Negative
77
N'chifukwa chiyani wangokhala wekha kupereka ziweruzo ndipo anthu onse ali chiimire pamaso pako kuyambira m'mawa mpaka madzulo?"
Negative
78
Atamuuza vutoli, Yesu anamuuza momveka bwino kuti: "Inu mumalambira chimene simuchidziwa."
Positive
79
Ndiponso sadzawayeretsa (kumachimo awo); ndipo iwo adzapeza chilango chopweteka.
Negative
80
monga mawu omveka, pamene khoma limodzi limaphimbidwa;
Negative
81
Ndithu ine ndikumganizira kuti ndi mmodzi wa abodza."
Negative
82
Mwachitsanzo, Solomo anachonderera Mulungu kuti aziyankha mapembedzero a olambira Ake.
Positive
83
mwa Mulungu ine ndimadaliramo; sindidzachita mantha.
Positive
84
Ndipo, ndithudi, ngati pali mwamuna mu aquarium iyi.
Negative
85
Iwo sayenera amafanana zovala zachimuna kapena zovala za osakhulupirira.
Negative
86
"Pamene m'bale wawo (Mneneri) Hûd adawafunsa kuti: "Kodi simuopa (Allah)?"
Positive
87
"Kufikira pamene adzatidzera (tsiku la Qiyâma, uku akulowetsedwa ku Moto).
Positive
88
Atate, ndipulumutseni Ine ku nthaŵi iyi."
Negative
89
"Mawa lino adzadziwa (tsiku lakuwatsikira chilango,) kuti ndiyani wabodza wodzitukumula (iwo kapena Swaleh).
Negative
90
"Nena: "Yendani pa dziko ndi kuona momwe Allah adayambitsira chilengedwe; kenako Allah adzaumba, kuumba kwina.
Positive
91
Chifukwa ndaona zonse zimene Labani wachita kwa inu.
Negative
92
Amphaka ngati dzina lawo limveka;
Positive
93
"Kotero alemekezeke Yemwe m'manja Mwake muli ulamuliro pa chinthu chilichonse; ndipo kwa Iye (ndiko) mudzabweerera nonse.
Positive
94
"Zimenezo nchifukwa chakuti iwo adakonda moyo wa dziko lapansi kwambiri kuposa wa pambuyo pa imfa; ndi kutinso Allah saongola anthu osakhulupirira.
Negative
95
M'nthaka muli zizindikiro kwa Otsimikiza, (Zosonyeza kuti Mulungu alipo).
Positive
96
ndipo zaka za moyo wako zidzakhala zochuluka.
Positive
97
Uchiteni mzinda uwu (wa Makka) kukhala wa mtendere; ndipo ndipatuleni ine ndi ana anga ku machitidwe opembedza mafano."
Positive
98
Zikomo...izo anali Old School.
Positive
99
End of preview. Expand in Data Studio

Chichewa Sentiment Corpus

Dataset Description

This dataset contains sentiment-labeled text data in Chichewa for binary sentiment classification (Positive/Negative). Sentiments are extracted and processed from the English meanings of the sentences using DistilBERT for sentiment classification. The dataset is part of a larger collection of African language sentiment analysis resources.

Dataset Statistics

  • Total samples: 834,916
  • Positive sentiment: 450225 (53.9%)
  • Negative sentiment: 384691 (46.1%)

Dataset Structure

Data Fields

  • Text Column: Contains the original text in Chichewa
  • sentiment: Sentiment label (Positive or Negative only)

Data Splits

This dataset contains a single split with all the processed data.

Data Processing

The sentiment labels were generated using:

  • Model: distilbert-base-uncased-finetuned-sst-2-english
  • Processing: Batch processing with optimization for efficiency
  • Deduplication: Duplicate entries were removed based on text content
  • Filtering: Only Positive and Negative sentiments retained for binary classification

Usage

from datasets import load_dataset

# Load the dataset
dataset = load_dataset("michsethowusu/chichewa-sentiments-corpus")

# Access the data
print(dataset['train'][0])

# Check sentiment distribution
from collections import Counter
sentiments = [item['sentiment'] for item in dataset['train']]
print(Counter(sentiments))

Use Cases

This dataset is ideal for:

  • Binary sentiment classification tasks
  • Training sentiment analysis models for Chichewa
  • Cross-lingual sentiment analysis research
  • African language NLP model development

Citation

If you use this dataset in your research, please cite:

@dataset{chichewa_sentiments_corpus,
  title={Chichewa Sentiment Corpus},
  author={Mich-Seth Owusu},
  year={2025},
  url={https://huggingface.co/datasets/michsethowusu/chichewa-sentiments-corpus}
}

License

This dataset is released under the MIT License.

Contact

For questions or issues regarding this dataset, please open an issue on the dataset repository.

Dataset Creation

Date: 2025-07-02 Processing Pipeline: Automated sentiment analysis using HuggingFace Transformers Quality Control: Deduplication, batch processing optimizations, and binary sentiment filtering applied

Downloads last month
0

Collection including michsethowusu/chichewa-sentiments-corpus